NYIMBO 138 Imvi Ndi Chisoti cha Ulemerero Sankhani Zoti Mumvetsere Imvi Ndi Chisoti cha Ulemerero Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Miyambo 16:31) 1. Pano tili ndi anthu Achikulire. Akukondabe M’lungu; Sanamusiye. Enatu umasiye Ukuwawawa Tate, atonthozeni, Alimbitseni. (KOLASI) Mumakumbukira Zochita zawo. Tate auzeni: “Mwachita bwino!” 2. Imvi za olungama Ndi zokongola. Zimasangalatsadi Tate Yehova. Ife tikumbukire Pa nthawi ina. Pa unyamata wawo Ankayesetsa. (KOLASI) Mumakumbukira Zochita zawo. Tate auzeni: “Mwachita bwino!” (Onaninso Sal. 71:9, 18; Miy. 20:29; Mat. 25:21, 23; Luka 22:28; 1 Tim. 5:1.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Imvi Ndi Chisoti cha Ulemerero IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Imvi Ndi Chisoti cha Ulemerero (Nyimbo 138) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Imvi Ndi Chisoti cha Ulemerero (Nyimbo 138) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016938/sign/wpub/1102016938_sign_sqr_xl.jpg sjj 138