NYIMBO 142 Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu Sankhani Zoti Mumvetsere Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Aheberi 6:18, 19) 1. Anthu akhala akuyenda mumdima. Ndipo sanapindule kalikonse. Zadziwika kuti anthu ochimwa; Kuvutika sangakuthetse. (KOLASI) Tiyeni tiimbe mokondwera! Poti Ufumu wa M’lungu wabwera. Yesu adzachotsadi zoipa; Chiyembekezochi n’chodalirika. 2. Uthenga womwe ukumveka ndi woti; “Tsiku la Mulungu layandikira.” Anthu sadzakhalanso ndi chisoni. M’lungu wathu timuimbira. (KOLASI) Tiyeni tiimbe mokondwera! Poti Ufumu wa M’lungu wabwera. Yesu adzachotsadi zoipa; Chiyembekezochi n’chodalirika. (Onaninso Sal. 27:14; Mlal. 1:14; Yow. 2:1; Hab. 1:2, 3; Aroma 8:22.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu (Nyimbo 142) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu (Nyimbo 142) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016942/sign/wpub/1102016942_sign_sqr_xl.jpg sjj 142