NYIMBO 143 Pitirizani Kugwira Ntchito, Kukhala Maso Komanso ndi Kudikira Sankhani Zoti Mumvetsere Pitirizani Kugwira Ntchito, Kukhala Maso Komanso ndi Kudikira Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Aroma 8:20-25) 1. Nthawi ya Mulungu wathu, Yayandikira kwambiri— Kutitu alamulire Umboni waoneka. (KOLASI) Pitirizani kukhala maso, Kuti mudzapeze moyo, Womwe M’lungu wakonza. 2. M’lungu anaika nthawi; Yoti Yesu agonjetse, Adani ake onsewa. Iye adzapambana. (KOLASI) Pitirizani kukhala maso, Kuti mudzapeze moyo, Womwe M’lungu wakonza. 3. Mavuto m’chilengedwechi, Akuchuluka kwambiri. Tiyembekeze Yehova, Adzatipulumutsa. (KOLASI) Pitirizani kukhala maso, Kuti mudzapeze moyo, Womwe M’lungu wakonza. (Onaninso Mat. 25:13; Luka 12:36.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Pitirizani Kugwira Ntchito, Kukhala Maso Komanso ndi Kudikira IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Pitirizani Kugwira Ntchito, Kukhala Maso Komanso ndi Kudikira (Nyimbo 143) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Pitirizani Kugwira Ntchito, Kukhala Maso Komanso ndi Kudikira (Nyimbo 143) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016943/sign/wpub/1102016943_sign_sqr_xl.jpg sjj 143