NYIMBO 147 Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha Sankhani Zoti Mumvetsere Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Salimo 37:29) 1. Mulungu watilonjeza. Moyo womwe sudzatha. ‘Ofatsa ’dzasangalala.’ Zidzachitikadi. (KOLASI) Tidzakhala ndithu, Ndi moyo wosatha. M’lungu walonjeza. Zidzachitika. 2. Paradaiso akubwera; Anthu adzamasuka. Kudzakhaladi mtendere, Wochoka kwa M’lungu. (KOLASI) Tidzakhala ndithu, Ndi moyo wosatha. M’lungu walonjeza. Zidzachitika. 3. Akufawo adzauka, Chisoninso chidzatha. Mulungu adzapukuta, Misozi ya anthu. (KOLASI) Tidzakhala ndithu, Ndi moyo wosatha. M’lungu walonjeza. Zidzachitika. (Onaninso Yes. 25:8; Luka 23:43; Yoh. 11:25; Chiv. 21:4.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha (Nyimbo 147) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha (Nyimbo 147) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016947/sign/wpub/1102016947_sign_sqr_xl.jpg sjj 147