NYIMBO 148 Yehova Amapereka Populumukira Sankhani Zoti Mumvetsere Yehova Amapereka Populumukira Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (2 Samueli 22:1-8) 1. Yehova ndinudi Mulungu wamoyo; M’chilengedwe chonse Mphamvu zaoneka. Palibe M’lungu wina angachite —zimene Inu mumachita. (KOLASI) Yehova ndiye pothawira pathu. Tidzaonadi kuti iye ndi Thanthwe. Tilengeze molimba mtima mphamvu zake. Yehova m’pothawira pathu, tim’tamande. 2. Zingwe za imfa zingandizungulire, ndidalira inu, “Mundipatse mphamvu, mundilimbitse mtima.” Mumve kulira kwanga “Ndibiseni M’lungu.” (KOLASI) Yehova ndiye pothawira pathu. Tidzaonadi kuti iye ndi Thanthwe. Tilengeze molimba mtima mphamvu zake. Yehova m’pothawira pathu, tim’tamande. 3. Mudzagunda ngati mabingu kumwamba. Adzanjenjemera; Adani anuwo. Mudzakhala chimene mukufuna kukhala Onse adzaona. (KOLASI) Yehova ndiye pothawira pathu. Tidzaonadi kuti iye ndi Thanthwe. Tilengeze molimba mtima mphamvu zake. Yehova m’pothawira pathu, tim’tamande. (Onaninso Sal. 18:1, 2; 144:1, 2.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Yehova Amapereka Populumukira IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Yehova Amapereka Populumukira (Nyimbo 148) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Yehova Amapereka Populumukira (Nyimbo 148) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016948/sign/wpub/1102016948_sign_sqr_xl.jpg sjj 148