NYIMBO 150 Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke Sankhani Zoti Mumvetsere Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Zefaniya 2:3) 1. Mitundu ya anthu Ikutsutsabe Yesu. Ulamuliro wa anthu Utha watero M’lungu. Ufumu wa M’lungu Ukulamuliradi. Yesu adzachotsa adani. Adzatha posachedwa. (KOLASI) Bweranitu kwa Yehova Kuti mudzapulumuke. Musakayike, Muzimumvera, Mukhale kumbali yake. Adzakupulumutsani Ndi mphamvu zake. 2. Anthu akusankha Kumvetsera uthenga. Timalalikira onse. Enatu amakana. Tikamavutika Tisakhale ndi mantha. M’lungu adzatisamalira Timukhulupirire. (KOLASI) Bweranitu kwa Yehova Kuti mudzapulumuke. Musakayike, Muzimumvera, Mukhale kumbali yake. Adzakupulumutsani Ndi mphamvu zake. (Onaninso 1 Sam. 2:9; Sal. 2:2, 3, 9; Miy. 2:8; Mat. 6:33.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke (Nyimbo 150) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke (Nyimbo 150) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016950/sign/wpub/1102016950_sign_sqr_xl.jpg sjj 150