NYIMBO 18 Tikuthokoza Chifukwa cha Dipo Sankhani Zoti Mumvetsere Tikuthokoza Chifukwa cha Dipo Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Luka 22:20) 1. Lero tabweratu, kwa inu Yehova, Chifukwa munatisonyezadi chikondi. Munapereka Mwana, wanu woyamba. Monga nsembe yoposa ina iliyonse. (KOLASI) Anafera anthu onse. Kuti tidzapulumuke. Tikuthokoza ndi mtima wonse, Inu M’lungu. 2. Mofunitsitsa Yesu anapereka. Nsembe ya dipo moti tikusangalala. Asanabwere kudzatipulumutsa. Sitinkayembekezera, moyo wosatha. (KOLASI) Anafera anthu onse. Kuti tidzapulumuke. Tikuthokoza ndi mtima wonse, Inu M’lungu. (Onaninso Aheb. 9:13, 14; 1 Pet. 1:18, 19.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Tikuthokoza Chifukwa cha Dipo IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Tikuthokoza Chifukwa cha Dipo (Nyimbo 18) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Tikuthokoza Chifukwa cha Dipo (Nyimbo 18) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016818/sign/wpub/1102016818_sign_sqr_xl.jpg sjj 18