NYIMBO 20 Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha Sankhani Zoti Mumvetsere Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (1 Yohane 4:9) 1. Yehova, tinali opanda tsogolo. Komano dipo lathandiza tonse. Tikudzipereka, kwa inu kosatha. Tiphunzitse ena, Akudziweninso. (KOLASI) Mwana wanu yekha, munamupereka. Tidzakuimbirani, za mphatsoyi kwamuyaya. 2. Chifundo chanucho ndi chachikuludi. Komanso timakonda dzina lanu. Yoposa zonsezi, ndi mphatso ya Yesu. Anatifera kuti tipulumuke. (KOLASI) Mwana wanu yekha, munamupereka. Tidzakuimbirani, za mphatsoyi kwamuyaya. (KUMALIZA) Yehova, Atate, tikuthokozatu. Mphatsoyi munatipatsadi kwamuyaya. (Onaninso Yoh. 3:16; 15:13.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha (Nyimbo 20) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha (Nyimbo 20) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016820/sign/wpub/1102016820_sign_sqr_xl.jpg sjj 20