NYIMBO 27 Ulemerero wa Ana a Mulungu Udzaonekera Sankhani Zoti Mumvetsere Ulemerero wa Ana a Mulungu Udzaonekera Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Aroma 8:19) 1. Posachedwa M’lungu wathu Odzozedwa ake, Adzawasonyeza kuti ndi ana akedi. (KOLASI) Khristu ndi odzozedwawo Adzapambanadi. Ulemerero wawonso Udzaonekera. 2. Posachedwa otsalira Adzaitanidwa. Khristu Mfumu ya mafumu, adzatenga onse. (KOLASI) Khristu ndi odzozedwawo Adzapambanadi. Ulemerero wawonso Udzaonekera. (VESI LOKOMETSERA) Limodzi ndi Mbuye wawo adzamenya nkhondo. Ukwati ndi Mbuye Yesu Udzachitikatu. (KOLASI) Khristu ndi odzozedwawo Adzapambanadi. Ulemerero wawonso Udzaonekera. (Onaninso Dan. 2:34, 35; 1 Akor. 15:51, 52; 1 Ates. 4:15-17.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ulemerero wa Ana a Mulungu Udzaonekera IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Ulemerero wa Ana a Mulungu Udzaonekera (Nyimbo 27) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ulemerero wa Ana a Mulungu Udzaonekera (Nyimbo 27) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016827/sign/wpub/1102016827_sign_sqr_xl.jpg sjj 27