NYIMBO 37 Kutumikira Yehova ndi Moyo Wathu Wonse Sankhani Zoti Mumvetsere Kutumikira Yehova ndi Moyo Wathu Wonse Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Mateyu 22:37) 1. Yehova Wamphamvuyonse, Inetu ndimakukondani. Mtima wanga wonse umafuna; Kukutumikirani. Malamulo anu ndimvera, Zofuna zanu ndichita. (KOLASI) Inu Yehova ndinu woyenera Kutumikiridwa. 2. Atate zomwe munalenga Zimakulemekezani. Ndi mphamvu zangatu zonse, Ndidzauza ena za inu. Ndithandizenitu Yehova, Kuti ndikhulupirike. (KOLASI) Inu Yehova ndinu woyenera Kutumikiridwa. (Onaninso Deut. 6:15; Sal. 40:8; 113:1-3; Mlal. 5:4; Yoh. 4:34.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kutumikira Yehova ndi Moyo Wathu Wonse IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Kutumikira Yehova ndi Moyo Wathu Wonse (Nyimbo 37) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kutumikira Yehova ndi Moyo Wathu Wonse (Nyimbo 37) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016837/sign/wpub/1102016837_sign_sqr_xl.jpg sjj 37