NYIMBO 38 Mulungu Adzakulimbitsa Sankhani Zoti Mumvetsere Mulungu Adzakulimbitsa Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (1 Petulo 5:10) 1. Panali chifukwa chimene Mulungu Anakupatsira choonadi. Anaona mtima wofuna kuchita Zabwino zomusangalatsadi. Unalonjeza kum’tumikira; Ndipo iye anakuthandiza. (KOLASI) Ndi magazi a Yesu Anakuwombola. Ndiwe wa Mulungu, adzakulimbitsa. Adzakutsogolera ndi mzimu woyera. Adzakulimbitsa adzakuteteza. 2. Mulungu anapereka Mwana wake; Amafunatu zikuyendere. Ngati Mwana wakeyo sanatimane Kukulimbitsa sangalephere. Chikondi chako sangaiwale; Sangasiye ndithu anthu ake. (KOLASI) Ndi magazi a Yesu Anakuwombola. Ndiwe wa Mulungu, adzakulimbitsa. Adzakutsogolera ndi mzimu woyera. Adzakulimbitsa adzakuteteza. (Onaninso Aroma 8:32; 14:8, 9; Aheb. 6:10; 1 Pet. 2:9.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mulungu Adzakulimbitsa IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Mulungu Adzakulimbitsa (Nyimbo 38) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mulungu Adzakulimbitsa (Nyimbo 38) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016838/sign/wpub/1102016838_sign_sqr_xl.jpg sjj 38