NYIMBO 58 Kufufuza Anthu Okonda Mtendere Sankhani Zoti Mumvetsere Kufufuza Anthu Okonda Mtendere Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Luka 10:6) 1. Yesu anatilamula kuti tiuze anthu uthenga. Amve mawu a Yehova. Ankakonda nkhosa za Mulungu. Ankazifufuza mwakhama tsiku lonse. Nyumba ndi nyumba, mumsewu Timauza aliyense, Kuti posachedwa mavuto atha. (KOLASI) Tifufuze okonda mtendere m’dzikoli. Tiwapeze Ofuna kupulumutsidwa. Tifufuze Paliponse. 2. Tifufuzabe anthu mwa khama. Alipo ambiri omwe tingathe kuwathandiza. Poti timawakonda kwambiri, Tibwererekonso Tikawalimbikitse. M’matauni, ndi m’midzinso, Tikapeza omvetsera, Timasangalala powaphunzitsa. (KOLASI) Tifufuze okonda mtendere m’dzikoli. Tiwapeze Ofuna kupulumutsidwa. Tifufuze Paliponse. (Onaninso Yes. 52:7; Mat. 28:19, 20; Luka 8:1; Aroma 10:10.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kufufuza Anthu Okonda Mtendere IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Kufufuza Anthu Okonda Mtendere (Nyimbo 58) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kufufuza Anthu Okonda Mtendere (Nyimbo 58) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016858/sign/wpub/1102016858_sign_sqr_xl.jpg sjj 58