NYIMBO 61 Pitani Patsogolo Mboninu Sankhani Zoti Mumvetsere Pitani Patsogolo Mboninu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Luka 16:16) 1. Olimba m’nthawi yamapeto ino Ndi atumiki olengeza uthenga. Mdyerekezi amawatsutsa, Ndi mphamvu za Yehova samagonja. (KOLASI) Ndiye pitani patsogolo mboninu. Sangalalani pogwira ntchito yake. Uzani onse zadziko latsopano Mmene mudzakhale madalitso. 2. Tisatengeke ndi moyo wofewa. Tizipewa kusangalatsa dzikoli. Tikane zochita za dziko Ndi kukhala okhulupirikabe. (KOLASI) Ndiye pitani patsogolo mboninu. Sangalalani pogwira ntchito yake. Uzani onse zadziko latsopano Mmene mudzakhale madalitso. 3. Ufumu wa M’lungu ukunyozedwa, Dzina lake loyera likudetsedwa. Tiyeni tiziliyeretsa. Tililengeze kumitundu yonse. (KOLASI) Ndiye pitani patsogolo mboninu. Sangalalani pogwira ntchito yake. Uzani onse zadziko latsopano Mmene mudzakhale madalitso. (Onaninso Eks. 9:16; Afil. 1:7; 2 Tim. 2:3, 4; Yak. 1:27.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Pitani Patsogolo Mboninu IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Pitani Patsogolo Mboninu (Nyimbo 61) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Pitani Patsogolo Mboninu (Nyimbo 61) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016861/sign/wpub/1102016861_sign_sqr_xl.jpg sjj 61