NYIMBO 71 Ndife Gulu Lankhondo la Yehova Sankhani Zoti Mumvetsere Ndife Gulu Lankhondo la Yehova Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Yoweli 2:7) 1. Ndife gulu lankhondo, La M’lungu wathu. Lotsogoleredwa ndi Mwana wake Yesu. Satana angatsutse, Tilalikabe. Ndife osaopa Olimba mtima. (KOLASI) Ndife gulu lankhondo. Tikulengeza: “Ufumu wayamba Kulamulira.” 2. Ndife anthu a M’lungu, Ofunafuna, Anthu omwe ndi nkhosa, Zosowa za M’lungu. Tifuna kuwapeza, N’kuwaphunzitsa, N’kuwalimbikitsa: “Tizisonkhana.” (KOLASI) Ndife gulu lankhondo. Tikulengeza: “Ufumu wayamba Kulamulira.” 3. Ndife gulu lankhondo, Lomvera Yesu, Lokonzekera nkhondo, Lolimbatu mtima. Koma tikhale tcheru, Kuti tisagwe. Zinthu zikavuta, Tisafooke. (KOLASI) Ndife gulu lankhondo. Tikulengeza: “Ufumu wayamba Kulamulira.” (Onaninso Aef. 6:11, 14; Afil. 1:7; Filim. 2.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ndife Gulu Lankhondo la Yehova IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Ndife Gulu Lankhondo la Yehova (Nyimbo 71) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndife Gulu Lankhondo la Yehova (Nyimbo 71) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016871/sign/wpub/1102016871_sign_sqr_xl.jpg sjj 71