NYIMBO 75 “Ine Ndilipo! Nditumizeni!” Sankhani Zoti Mumvetsere “Ine Ndilipo! Nditumizeni!” Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Yesaya 6:8) 1. Lero anthu akunyoza Dzina loyera la M’lungu. Ena amati n’ngwankhanza. Enanso: “Kulibe M’lungu.” Ndani adzaliyeretsa, Dzina la Yehova M’lungu? (KOLASI 1) ‘Ndilipo! Nditumizeni! Ndidzaimbira inuyo. Ndi mwayi waukulu, Mbuye. Ine! Nditumizeni!’ 2. Anthu osaopa M’lungu; Akumati akuchedwa. Amalambira mafano, Ena eti Kaisara. Ndani adzawachenjeza Za nkhondo ya M’lungu wathu? (KOLASI 2) ‘Ndilipo! Nditumizeni! N’dzachenjeza mosaopa. Ndi mwayi waukulu, Mbuye. Ine! Nditumizeni!’ 3. Anthu ofatsa ’kulira Zoipa zikuchuluka. Iwo amafunitsitsa Choonadi chomasula. Ndani adzawatonthoza? Ndani adzawathandiza? (KOLASI 3) ‘Ndilipo! Nditumizeni! Ndidzaphunzitsa ofatsa. Ndi mwayi waukulu, Mbuye. Ine! Nditumizeni!’ (Onaninso Sal. 10:4; Ezek. 9:4.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena “Ine Ndilipo! Nditumizeni!” IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA “Ine Ndilipo! Nditumizeni!” (Nyimbo 75) Chinenero Chamanja cha ku Malawi “Ine Ndilipo! Nditumizeni!” (Nyimbo 75) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016875/sign/wpub/1102016875_sign_sqr_xl.jpg sjj 75