NYIMBO 79 Athandizeni Kukhala Olimba Sankhani Zoti Mumvetsere Athandizeni Kukhala Olimba Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Mateyu 28:19, 20) 1. Kuphunzitsa nkhosa za M’lungu Ndi mwayi wapadera. Yehova wawatsogolera Amakonda cho’nadi. (KOLASI) Yehova tikupemphatu Kuti muziwateteza. Mwa Yesu tikupemphani: Athandizenibe Akhale olimba. 2. Mayesero akawagwera, Tinkawapempherera. Tinawaphunzitsa mwakhama; Pano adalitsidwa. (KOLASI) Yehova tikupemphatu Kuti muziwateteza. Mwa Yesu tikupemphani: Athandizenibe Akhale olimba. 3. Akhale okudalirani, Inu M’lungu ndi Yesu. Apirire pamayesero, Akalandire moyo. (KOLASI) Yehova tikupemphatu Kuti muziwateteza. Mwa Yesu tikupemphani: Athandizenibe Akhale olimba. (Onaninso Luka 6:48; Mac. 5:42; Afil. 4:1.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Athandizeni Kukhala Olimba IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Athandizeni Kukhala Olimba (Nyimbo 79) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Athandizeni Kukhala Olimba (Nyimbo 79) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016879/sign/wpub/1102016879_sign_sqr_xl.jpg sjj 79