NYIMBO 81 Moyo wa Mpainiya Sankhani Zoti Mumvetsere Moyo wa Mpainiya Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Mlaliki 11:6) 1. M’mawa uliwonse, tulo tisanathe, Timadzuka n’kupita kolalikira uthenga. Ndipo Mulungu amatitsogolera Timakondwa anthu akamamvetsera uthenga. (KOLASI) Tinasankha, kutumikira Yehova. Timachita zofuna zake. Tipitirizabe kulalikiraku, Tikatero timasonyeza Chikondi. 2. Pofika madzulo, timatopa ndithu, Komabe timapeza chimwemwe potumikira. Madalitso Yehova amatipatsa Nthawi zonse timamuthokoza potithandiza. (KOLASI) Tinasankha, kutumikira Yehova. Timachita zofuna zake. Tipitirizabe kulalikiraku, Tikatero timasonyeza Chikondi. (Onaninso Yos. 24:15; Sal. 92:2; Aroma 14:8.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Moyo wa Mpainiya IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Moyo wa Mpainiya (Nyimbo 81) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Moyo wa Mpainiya (Nyimbo 81) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016881/sign/wpub/1102016881_sign_sqr_xl.jpg sjj 81