NYIMBO 9 Yehova Ndi Mfumu Yathu Sankhani Zoti Mumvetsere Yehova Ndi Mfumu Yathu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Salimo 97:1) 1. Kondwa lemekeza Yehova, Kumwamba kulengeza chilungamo. Mosangalala tiimbire Mulungu, Tiuze onse ntchito zake. (KOLASI) Kumwamba kukondwe, Dziko likondwere, Chifukwa Yehova ndi Mfumu. Kumwamba kukondwe, Dziko likondwere, Chifukwa Yehova ndi Mfumu. 2. Nena za kukwezeka kwake, Chifukwa ndiye wotipulumutsa. Yehova, tiyenera kumutamanda. Tiyenitu timugwadire. (KOLASI) Kumwamba kukondwe, Dziko likondwere, Chifukwa Yehova ndi Mfumu. Kumwamba kukondwe, Dziko likondwere, Chifukwa Yehova ndi Mfumu. 3. Wakhazikitsatu Ufumu. Waika Mwana wake pampandowo. Milungu yabodza ichite manyazi, Titamande Yehova yekha. (KOLASI) Kumwamba kukondwe, Dziko likondwere, Chifukwa Yehova ndi Mfumu. Kumwamba kukondwe, Dziko likondwere, Chifukwa Yehova ndi Mfumu. (Onaninso 1 Mbiri 16:9; Sal. 68:20; 97:6, 7.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Yehova Ndi Mfumu Yathu IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Yehova Ndi Mfumu Yathu (Nyimbo 9) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Yehova Ndi Mfumu Yathu (Nyimbo 9) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016809/sign/wpub/1102016809_sign_sqr_xl.jpg sjj 9