NYIMBO 99 Abale Ambirimbiri Sankhani Zoti Mumvetsere Abale Ambirimbiri Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Chivumbulutso 7:9, 10) 1. Abale ambirimbiri. Inde ochuluka. Aliyense ndi mboni Yokhulupirika. Tilipodi ambiri. Tikuchulukabe. Tachokera m’mayiko onse Ndi mitundu yonse. 2. Abale ambirimbiri. Timalalikira Uthenga wabwinowu Kwa ofuna kumva. Pamene tafooka Yesu atipatsa Mpumulo ndi mphamvu zambiri. Sitimada nkhawa. 3. Abale ambirimbiri. Timatetezedwa Potumikira M’lungu Padziko lapansi. Tilipodi ambiri. Timalalikira. Timagwira ntchito ndi M’lungu Pomutumikira. (Onaninso Yes. 52:7; Mat. 11:29; Chiv. 7:15.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Abale Ambirimbiri IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Abale Ambirimbiri (Nyimbo 99) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Abale Ambirimbiri (Nyimbo 99) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016899/sign/wpub/1102016899_sign_sqr_xl.jpg sjj 99