Gwiritsani Ntchito Mphamvu Zanu Potumikira Yehova YAMBANI Gwiritsani Ntchito Mphamvu Zanu Potumikira Yehova Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Ulitu mwana, zinkaphwekako Kuchitatu zoyenera. Unkakondanso kulalikira, N’kupemphera nthawi zonse. (KUKONZEKERA KOLASI) Koma pomwe ukukula zinthu zingasinthe. Ungakanike kugogoda m’makomo mu ‘tumiki. Koma pomwe watalika chonde usasiye Kutumikira Yehova, Adzakudalitsa. (KOLASI) M’nyumba ya Yehova uli ndi malo, Akuthandiza. Ungamupatse Yehova zambiritu. M’lungu amaona, Amakukonda. 2. Pano wakula, zinthu zasinthadi, Mayesero ayambanso. Nkhawa nazo zachulukadi Pemphera, M’lungu amamva. (KUKONZEKERA KOLASI) Pomwetu wakula uzichita zimene Umaphunzira, udzasangalala ndithu. Pomwe ukufuna kuti usankhe zochita, Usaiwale Yehova, Adzakudalitsa. (KOLASI) M’nyumba ya Yehova uli ndi malo, Akuthandiza. Ungamupatse Yehova zambiritu. M’lungu amaona, Amakukonda. (VESI LOKOMETSERA) M’tumikire ndi mphamvu zako. N’zabwinodi, sungadzadandaule. (KOLASI) M’nyumba ya Yehova uli ndi malo, Akuthandiza. Ungamupatse Yehova zambiritu. M’lungu amaona, Amakukonda. (VESI LOKOMETSERA) M’tumikire ndi mphamvu zako. N’zabwinodi, sungadzadandaule. M’tumikire ndi mphamvu zako. N’zabwinodi, sungadzadandaule. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Gwiritsani Ntchito Mphamvu Zanu Potumikira Yehova NYIMBO ZATHU Gwiritsani Ntchito Mphamvu Zanu Potumikira Yehova Chinenero Chamanja cha ku Malawi Gwiritsani Ntchito Mphamvu Zanu Potumikira Yehova https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014355/univ/art/1014355_univ_sqr_xl.jpg