Dziko Latsopano Lili Pafupi YAMBANI Dziko Latsopano Lili Pafupi Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1.Mbalametu zikuimba, Mitambo ikuyenda. Mukudutsa pachidikha Ndipo dzuwa likuwalanso. Akufa akuuka, Ngati mukungolota. Dziko la Paradaiso Linalidi pafupi. 2.Muchidikha muli nyumba Ina ili pa phiri. Anthu akuimba nyimbo Mumtsinje madzi akuyenda. Mbewu zachanso m’minda. Ndi nthawi yokolora. Dziko lokongolali Linalidi pafupi. (VESI LOKOMETSERA) Tiziuza anzathunso Zomwe tikuyembekeza. Sikudzakhala kulira. Zinthu zonse n’zatsopano. 3.Anthu akusangalala Kafungo ka zomera. Mukuitanitsa ‘nzanu Pamene tsiku likuyamba. Tikuthokoza Yehova, Posonyeza chikondi. Madalitso onsewa Analidi pafupi. (VESI LOKOMETSERA) Ndikaona nkhope yanu, Ikumandimwetulira. Sindinkaganiza n’komwe Kuti tidzakumananso. 4.Dziko latsopano Ndikuliyembekeza. Ndi lonjezo la Yehova. Ndipo lidzakwaniritsidwa. Ndikaganizira izi Sindimadanso nkhawa. Chifukwatu dzikolo, Lilitu pafupi zedi. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Dziko Latsopano Lili Pafupi NYIMBO ZATHU Dziko Latsopano Lili Pafupi Chinenero Chamanja cha ku Malawi Dziko Latsopano Lili Pafupi https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014225/univ/art/1014225_univ_sqr_xl.jpg