Ganizira Nthawiyo YAMBANI Ganizira Nthawiyo Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Pano moyo ndi wovuta. Chakudya n’choperewera. N’katseka maso ndimaona Ndili m’dziko latsopano. (KOLASI) Taganizira nthawi imene, Moyo udzakhaladi wabwino. Taganizira pomwe tidzati, “Zikomo moyo wabwino zonse zabwino.” 2. Ndinabadwatu wogontha, Masowa sakuonanso. Makutu adzayamba kumva. Maso anga adzaona. (KOLASI) Taganizira nthawi imene, Moyo udzakhaladi wabwino. Taganizira pomwe tidzati, “Zikomo moyo wabwino zonse zabwino.” (VESI LOKOMETSERA) Sin’ngayende koma ndikudziwa. Tsiku lina ndidzathamanga! (KOLASI) Taganizira nthawi imene, Moyo udzakhaladi wabwino. Ganizira chisangalalo chake Tsiku lililonse n’labwino. (KOLASI) Taganizira nthawi imene, Moyo udzakhaladi wabwino. Taganizira pomwe tidzati, “Zikomo moyo wabwinowu.” Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ganizira Nthawiyo NYIMBO ZATHU Ganizira Nthawiyo Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ganizira Nthawiyo https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014272/univ/art/1014272_univ_sqr_xl.jpg