Muziteteza Maganizo Anu YAMBANI Muziteteza Maganizo Anu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Ndimafuna n’zimumvera, Komatu ndimavutika— Ndikumaona ngati Ndikuchita zochepa. Usiku ndimapemphera, Paja ndi zomwe munandiuza. N’kayamba kuda nkhawa, Yehova paja munati (KOLASI) Ndiziteteza mtima wangawu, N’ganizire zabwinodi. N’saganizire zofo’ketsa. Ndidzapezatu mtendere ndithu. 2. Ndimafuna n’zimumvera, Koma ndimatopa ndi nkhawa. Pena ndimamva ngati M’lungu sangandikonde. Kukacha ndikatuluka Ndimauza ena za tsogolo. Nkhawa zanga n’kuchepa. Yehova muman’teteza. (KOLASI) Ndiziteteza mtima wangawu, N’ganizire zabwinodi. N’saganizire zofo’ketsa. Ndidzapezatu mtendere ndithu. Mtenderedi. (VESI LOKOMETSERA) Ndizichotsa maganizo Omwetu ndi ofo’ketsa. N’sade nkhawa, n’sakaikire M’lungu zikomo, pon’thandiza kuti N’samade nkhawa. (KOLASI) Ndiziteteza mtima wangawu, N’ganizire zabwinodi. N’saganizire zofo’ketsa. Ndidzapezatu mtendere ndithu. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Muziteteza Maganizo Anu NYIMBO ZATHU Muziteteza Maganizo Anu Chinenero Chamanja cha ku Malawi Muziteteza Maganizo Anu https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014346/univ/art/1014346_univ_sqr_xl.jpg