Ndiwe Wekha YAMBANI Ndiwe Wekha Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Ndiwetu Munthu wapadera. Inetu Ndimakukonda. Makhalidwe ako Aman’sangalatsa. Yehovatu Adzatidalitsa. Ndimamvatu bwino Umandithandiza. Ndiwe waulemu Umandikondadi. (KOLASI) Tikamagwirizana Chikondi chimakula. Tithokoze M’lungu, timakondana. Ndiwe wekha. 2. Wanga ndiwe wekha. Umandimvetsera. Limodzitu, Timalalikira. Ndimamvatu bwino Umandikondadi. Ulipotu wekha— Ndimasangalala. (KOLASI) Tikamagwirizana Chikondi chimakula. Tithokoze M’lungu, timakondana. Ndiwe wekha. Tikamagwirizana Chikondi chimakula. Tithokoze M’lungu, timakondana. Ndiwe wekha, Ndiwe wekha, Wanga. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ndiwe Wekha NYIMBO ZATHU Ndiwe Wekha Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndiwe Wekha https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014333/univ/art/1014333_univ_sqr_xl.jpg