Ngati Mwana YAMBANI Ngati Mwana Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Yesutu anati Tikhale ngati ana, M’dzikolitu anthu ndi onyada, Tikhaletu ngati mwana. Kuona ena mmene Yehova amawaonera. (KOLASI) Ngati mwana, tizikondana kwambiri, Tione zabwinotu mwa ‘bale athu. Ngati mwana, tikhale okoma mtima, Tisamaone mavuto mwa anzathu. 2. Pamene tikukula M’dziko limene n’loipa, Tingamakaikiretu ena, Zolinga, n’zonena zawo. Sizophweka kuona ena kukhala otiposa. (KOLASI) Ngati mwana, tizikondana kwambiri, Tione zabwinotu mwa ‘bale athu. Ngati mwana, tikhale okoma mtima, Tisamaone mavuto mwa anzathu. Ngatitu mwana. (VESI LOKOMETSERA) Potumikira, Yehova M’lungu, Timapezadi Chisangalalo, Tikumbukire M’dziko lonyadali, Tizikhalatu ngati mwana. (KOLASI) Ngati mwana, tizikondana kwambiri, Tione zabwinotu mwa ‘bale athu. Ngati mwana, tikhale okoma mtima, Tisamaone mavuto mwa anzathu. Ngatitu mwana. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ngati Mwana NYIMBO ZATHU Ngati Mwana Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ngati Mwana https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014327/univ/art/1014327_univ_sqr_xl.jpg