“Timakobidi Tiwiri” YAMBANI “Timakobidi Tiwiri” Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu 1. Tochepa N’tomwe ali nato. Enatu Akupereka zambiri zedi Ndipo iye Akudzimva wachabe. Kodi M’lungu wake Angalandire tochepa? (KOLASI) Kaya n’tochepa, Tiperekebe Ndipo M’lungu alandira. Iye ndi wamkulu Kuposa anthufe, Kuposa mitima yathu. Timpatse. 2. Kalekale Zinkamuyenderadi. Ankapereka Zochulukanso, anali ndi mphamvu. Pano zochepa N’zomwe angakwanitse Koma kwa Yehova Zochepazo ndi zochuluka. (KOLASI) Kaya n’tochepa, Tiperekebe Ndipo M’lungu alandira. Iye ndi wamkulu Kuposa anthufe, Kuposa mitima yathu. Timpatse. (VESI LOKOMETSERA) Amamvetsatu tikapereka Zochepa kapena zochuluka. Sadzatiiwala. (KOLASI) Kaya n’tochepa, Tiperekebe Ndipo M’lungu alandira. Iye ndi wamkulu Kuposa anthufe, Kuposa mitima yathu. Tim’patse. Tim’patse zomwe tingathe. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena “Timakobidi Tiwiri” NYIMBO ZATHU “Timakobidi Tiwiri” Chinenero Chamanja cha ku Malawi “Timakobidi Tiwiri” https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014373/univ/art/1014373_univ_sqr_xl.jpg