Tiziyamikira Chilengedwe cha Mulungu YAMBANI Tiziyamikira Chilengedwe cha Mulungu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Maluwa ’kukula m’mwamba mwa phiri, Mapiri akukongola chapatali, Kadzuwanso kakuwala bwino, Mbalame zikuuluka. (KUKONZEKERA KOLASI) N’napangidwa Modabwitsa Kodi nditani Kuti ndim’thokoze? (KOLASI) Ndizimuthokoza, Ndimuuze M’lungu Zikomotu Amatikondadi. N’kayang’ana, N’kuziganizira ntchito za Yehova. Ndim’thokoze pa chilichonse. Ndiziyamikira. Ndiziyamikira. 2. Kumwamba kukuchita kukongola, Mitundu yokongola mochititsa chidwi. Kaphokoso ka mtsinje kotsitsimula, Nyenyezi ndi mwezi zikuwala. (KUKONZEKERA KOLASI) N’napangidwa Modabwitsa Ndadziwa zochita Kuti ndim’thokoze. (KOLASI) Ndizimuthokoza, Ndimuuze M’lungu Zikomotu Amatikondadi. N’kayang’ana, N’kuziganizira ntchito za Yehova, Ndim’thokoze pa chilichonse. Ndiziyamikira. (VESI LOKOMETSERA) Ndaona nzeru ndi mphamvu, Ubwino wanu m’zonse, N’chikondi chanu. Ndikuthokoza; Ndiziyamikira. (KOLASI) Ndizimuthokoza, Ndimuuze M’lungu Zikomotu Amatikondadi. N’kayang’ana, N’kuziganizira ntchito za Yehova, Ndim’thokoze pa chilichonse. Ndiziyamikira. Ndiziyamikira. Tiziyamikira. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Tiziyamikira Chilengedwe cha Mulungu NYIMBO ZATHU Tiziyamikira Chilengedwe cha Mulungu Chinenero Chamanja cha ku Malawi Tiziyamikira Chilengedwe cha Mulungu https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1014311/univ/art/1014311_univ_sqr_xl.jpg