Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Zokhudza Mboni za Yehova

Gawo lino likuthandizani ngati mukufuna kulankhula nafe, kufika pamisonkhano yathu, kupempha munthu woti aziphunzira nanu Baibulo kapenanso ngati mukungofuna kudziwa zambiri zokhudza ife. Tikukupemphaninso kuti mubwere kudzaona malo kumaofesi athu kuti mudziwe mmene ntchito yathu imayendera.

Onaninso: Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Zotani?

Zimene Timakhulupirira Komanso Kuchita

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri

Pezani mayankho omveka bwino a mafunso amene anthu ambiri amakonda kufunsa.

Zochitika pa Moyo wa a Mboni za Yehova

Onani zimene zimachitikira a Mboni za Yehova akamayesetsa kulola kuti Baibulo lizitsogolera maganizo, zoyankhula ndi zochita zawo.

Zimene a Mboni za Yehova Amachita

Ife a Mboni za Yehova tikupezeka m’mayiko oposa 230 ndipo ndife osiya zikhalidwe komanso mitundu. N’kutheka kuti mumatidziwa bwino chifukwa cha ntchito yathu yolalikira, koma timathandizanso anthu a m’dera lathu m’njira zina zambiri.

Mboni za Yehova padziko lonse

Werengani kuti mudziwe mmene a Mboni za Yehova alili ogwirizana padziko lonse.

Yambani Kuphunzirani Baibulo Popanda Kulipira

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo—Vidiyo Yathunthu

Baibulo likuthandiza anthu ambirimbiri padziko lonse lapansi kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri. Kodi inunso mungakonde?

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.

Pemphani Kuti Tidzakuyendereni

Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova.

Misonkhano ndi Zochitika Zina

Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

Onani mkati mwa Nyumba ya Ufumu kuti mudziwe zimene zimachitika.

Fikani Pamsonkhano

Dziwani zambiri zokhudza misonkhano yathu. Pezani malo apafupi amene kumachitikira misonkhano yathu.

Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu

Chaka chilichonse anthu mamiliyoni ambiri amasonkhana pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu. Tikukuitanani ku mwambowu kuti mudzadziwe mmene imfa ya Yesu imakukhudzirani.

Zokhudza Mboni za Yehova Padziko Lonse

  • Mayiko amene a Mboni za Yehova amalambira Mulungu​—239

  • Mboni za Yehova padziko lonse​—8,816,562

  • Maphunziro a Baibulo aulere​—7,281,212

  • Anthu amene anapezeka pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu​—20,461,767

  • Mipingo​—118,177