N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira? YAMBANI N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Anthu ambiri amaona kuti mtanda ndi chizindikiro chimene Akhristu padziko lonse lapansi amagwiritsa ntchito. Ngakhale kuti ifenso a Mboni za Yehova ndi Akhristu, sitigwiritsa ntchito mtanda polambira. N’chifukwa chiyani zili choncho? Chifukwa chimodzi n’chakuti Baibulo limasonyeza kuti Yesu sanafere pamtanda koma anafera pamtengo umodzi woongoka. Komanso Baibulo limachenjeza Akhristu mwamphamvu kuti “thawani kupembedza mafano,” omwe akuphatikizapo kugwiritsa ntchito mtanda polambira.—1 Akorinto 10:14; 1 Yohane 5:21. Komanso n’zochititsa chidwi kuti Yesu anati: “Mwakutero, onse adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga, ngati mukukondana.” (Yohane 13:34, 35; Machitidwe 10:39) Zimene Yesu ananenazi zikuonetseratu kuti otsatira ake enieni adzadziwika ndi kusonyezana chikondi chenicheni, osati kugwiritsa ntchito mtanda kapena zizindikiro zina. Nkhani Zina Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi Mfundo Zofunika za M'Baibulo—Mavidiyo Kodi Mulungu Amafuna Kuti Anthu Azigwiritsa Ntchito Zizindikiro Pomulambira? Kodi zingatithandize kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu yemwe sitingamuone? ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA Yambani kuphunzira Baibulo Phunzirani Baibulo kwaulere, mochita kukambirana ndi mphunzitsi wanu. Sindikizani Patsani ena Patsani ena N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira? MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira? Chinenero Chamanja cha ku Malawi N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502013309/univ/art/502013309_univ_sqr_xl.jpg