Mfundo Zachidule—Croatia
- 4,038,000—Chiwerengero cha anthu
- 4,687—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 57—Mipingo
- Pa anthu 870 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
Zagreb, Croatia—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda mumsewu wotchedwa Ilica Street
Ku Rovinj m’dziko la Croatia—Akuphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?
Mu mzinda wa Zagreb ku Croatia—Akugawira kapepala ka Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?
Mu mzinda wa Zagreb ku Croatia—Akulalikira uthenga wopatsa chiyembekezo umene umapezeka m’Baibulo
Pula, Croatia—Akugawira kapepala kakuti Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo? pafupi ndi bwalo lamasewero la ku Rome.
M’tawuni ya Kaštel Gomilica, ku Dalmatia, Croatia—Akugawira kabuku kofotokoza Baibulo kwa munthu wogwira ntchito kudoko pa nthawi yake yopuma