Mboni za Yehova Padziko Lonse

Malta

  • Birgu, Malta​—Akugawira kapepala kakuti, Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?

Mfundo Zachidule—Malta

  • 542,000—Chiwerengero cha anthu
  • 877—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 11—Mipingo
  • Pa anthu 643 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi