Mboni za Yehova Padziko Lonse

Tanzania

  • Mudzi wa Ngibao kufupi ndi mzinda wa Arusha, Tanzania-Akugawira kabuku kakuti  Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha kwa Amasai

Mfundo Zachidule—Tanzania

  • 67,438,000—Chiwerengero cha anthu
  • 20,846—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 417—Mipingo
  • Pa anthu 3,392 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi