Nkhani za Padziko Lonse
Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2022
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tipitirizebe kukhala maso mwauzimu.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 10 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti lokhudza mliri wa COVID-19 komanso njira za mmene tingagwiritsire ntchito nthawi yathu mwanzeru
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 9 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zolimbikitsa komanso muli vidiyo yosonyeza zimene abale ndi alongo afotokoza zokhudza pulogalamu yongoyeserera yoyambiranso kusonkhana pamasom’pamaso.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti komanso akulengeza za lemba lachaka cha 2022.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tipitirizebe kukhala ogwirizana.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 6 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zolimbikitsa achikulire komanso mmene ntchito ya zomangamanga ikuyendera.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 5 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zolimbikitsa zomwe zingathandize mabanja kuti akwanitse kupirira pa nthawi ya mliriyi.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza zomwe zachitikira abale athu komanso akufotokoza mfundo zolimbikitsa zosonyeza mmene Yehova akutithandizira kukhalabe opirira ngakhale kuti tikukumana ndi mavuto.
Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza lipoti komanso zochitika zomwe zikusonyeza kuti Yehova akudalitsa ntchito yathu yolalikira ngakhale kuti kuli mliri.