Nkhani za Padziko Lonse
Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2021
M’bale Wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo komanso zitsanzo zolimbikitsa zomwe zikusonyeza kuti Yehova akudalitsa abale ndi alongo pabeteli pa nthawi ya mliriyi
Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2021
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza zitsanzo zolimbikitsa zosonyeza kuti ntchito yolalikira ikuyenda bwino pa nthawi ya mliriyi.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 9 la 2020
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza chifukwa chake tiyenera kupitirizabe kukhala osamala komanso zimene tingachite kuti tidziteteze ndiponso titeteze anthu ena ku mliri wa COVID-19.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2020
A Governing Body member explains how Bible prophecy can help us to endure during the pandemic.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2020
A Governing Body member highlights how young ones can cope with challenges resulting from the pandemic.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 6 la 2020
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mmene takhala tikulandirirabe chakudya chauzimu ngakhale kuti kuli mliri.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 5 la 2020
Wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza njira zimene Yehova watisamalirira mwachikondi pa nthawi ya mliriyi.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2020
M’bale wina wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zimene gulu lizitsatira posankha zochita pa nkhani yoyambiranso kuchita zinthu zina zokhudza kulambira.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 3 la 2020
Tamvani zimene Yehova anachita powathandiza kuti amvetsere nkhani yapadera komanso kuti achite mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye.