Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kuchita Chibwenzi

Kulikonse kumene mungapite, mumaona anthu omwe ali pa chibwenzi. Kodi inuyo ndi okonzeka kukhala pa chibwenzi? Ngati ndi choncho, mungatani kuti mupewe kulakwitsa zinthu komanso kuti musankhe zinthu mwanzeru, zomwe zingathandize kuti mudzakhale ndi banja losangalala?

Before Dating

Kodi N’kungocheza Kapena Kukopana?

Nkhani imene munthu wina angaione ngati yocheza, wina angaione ngati yomukopa. Mungatani kuti muzipewa kutumiza mameseji olakwika?

Zofunika Kuganizira pa Nkhani ya Chibwenzi

Ngati mukukayikira kuti munthu winawake amakukondani, yankhani mafunso awa.

Musamapitirire Malire

Muzitumiza mameseji oyenera kwa anzanu amene si amuna kapena akazi anu.

While Dating

Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo?

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe tanthauzo la kutengeka maganizo ndiponso chikondi chenicheni.

Kodi Baibulo Limavomereza Kuti Mwamuna ndi Mkazi Azikhalira Limodzi Asanakwatirane?

Malangizo ochokera kwa Mulungu amatithandiza kudziwa zimene tingachite kuti tikhale ndi banja logwirizana ndipo anthu amene amatsatira mfundo zake zinthu zimawayendera bwino nthawi zonse.

Breakups

Zomwe Zingakuthandizeni Ngati Chibwenzi Chatha

Mfundo zomwe zili mu zochitazi zikuthandizani kuti muzisangalalabe ngakhale kuti chibwenzi chatha.