Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kugonana

Kugonana pakokha si kolakwika, komabe timafunika kulamulira zilakolako zathu. Kodi mungakwanitse bwanji kukhala odziletsa popeza kuti m’dzikoli anthu ambiri amakonda zachiwerewere?

The Bible’s View

Mmene Mungafotokozere Zimene Mumakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana

Nthawi zina aliyense amafunika kufotokoza zimene amakhulupirira. Gwiritsani ntchito nkhani yakuti “Zoti Muchite,” pokonzekera mmene mungafotokozere zimene mumakhulupirira molimba mtima.

Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Kukambirana nkhani ngati izi kumakhala kovuta. Tsambali lingakuthandizeni kuti muzifotokoza mwanzeru komanso mosamala maganizo anu pa nkhani ya kugonana kwa amuna kapena akazi okhaokha.

Maintaining Virtue

Ndingatani Ngati Anzanga Akundikakamiza Kuti Ndichite Zachiwerewere?

Pali mfundo zitatu za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni kukana mayesero.

Muziganizira Kufunika kwa Zomwe Mumakhulupirira: Pa Nkhani ya Kudzisunga

Tsambali lingakuthandizeni kuti muzisankha mwanzeru ngakhale zinthu zitavuta.

Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula

N’chifukwa chiyani pulogalamu yoteteza kuonera zolaula pa Intaneti siyokwanira?