Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Makhalidwe Oipa

Makhalidwe oipa savuta kuwayamba koma zimavuta kuwasiya. Gawo lino lifotokoza ena mwa makhalidwe oipa komanso zimene mungachite kuti muwasiye n’kuyamba kuzolowera kuchita zinthu zabwino.

Kulankhulana

Kodi Ndingatani Kuti Ndithetse Miseche?

Ngati anzanu ayamba kulankhula zonyoza kapena zoipa za anthu ena, musayankhire nawo koma sinthani nkhaniyo!

Addictions

Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula

N’chifukwa chiyani pulogalamu yoteteza kuonera zolaula pa Intaneti siyokwanira?

Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta

Anthu ambiri amasuta kapena kuvepa. Komabe ena asiya ndipo enanso akufunitsitsa kusiya. N’chifukwa chiyani akuchita zimenezi? Kodi kusuta kungawonongedi moyo wanu?

Time Management

Zimene Achinyamata Amanena pa Nkhani Yochita Zinthu Mozengereza

Imvani zimene achinyamata anzanu akufotokoza pa za kuipa kochita zinthu mozengereza ndiponso ubwino wochita zinthu mosazengereza.