Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Zipangizo Zamakono

Ngati muli ndi foni kapena zipangizo zina zamakono, mungadabwe kuti mukumazigwiritsa ntchito kwa nthawi yaitali kuposa mmene mumaganizira. Kodi mungatani kuti muzidziletsa pa nkhani yogwiritsa ntchito zipangizozi?

Electronic Devices

Magemu Amene Ndimasewera pa Zipangizo Zamakono

Mafunsowa angakuthandizeni kudziwa ngati magemu amene mumasewera ali abwino kapena ayi.

Kodi Zipangizo Zanu Zimakulamulirani Kapena Mumazilamulira?

Masiku ano anthu ambiri akugwiritsa ntchito zipangizo zamakono, koma musamalole kuti zimenezi zizilamulira moyo wanu. Nanga mungadziwe bwanji kuti mwayamba kukonda kwambiri zipangizo zanu? Ngati mulidi ndi vuto limeneli kodi mungatani kuti mulithetse?

Social Media

Muzichita Zinthu Mosamala Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti

Chitani zinthu mosamala mukamacheza ndi anzanu pa Intaneti.

Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu

Onani zimene zingakuthandizeni kukhala osamala musanatumize zithunzi.

Zimene Mungachite Kuti Anthu Asiye Kukuvutitsani pa Intaneti

Tsambali likuthandizani kuzindikira ubwino ndi mavuto a njira zosiyanasiyana komanso kuti muthe kudziwa zoyenera kuchita kuti winawake asamakuvutitseni pa Intaneti.