ZOTI MUCHITE Ngati Bambo Kapena Mayi Anu Akudwala YAMBANI Tsambali lingakuthandizeni kudziwa zimene mungachite mukamathandiza wodwala. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yosamalira Makolo Achikulire? Baibulo limafotokoza zimene amuna ndi akazi ena anachita m’mbuyomo posamalira makolo awo achikulire. Lilinso ndi mfundo zomwe zingathandize anthu omwe akusamalira makolo achikulire panopa. ESSENTIAL BIBLE TEACHINGS N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika? Anthu ambiri amafuna kudziwa kuti n’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri. Baibulo limapereka yankho logwira mtima pa nkhaniyi. Patsani ena Patsani ena Ngati Bambo Kapena Mayi Anu Akudwala ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Ngati Bambo Kapena Mayi Anu Akudwala Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ngati Bambo Kapena Mayi Anu Akudwala https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502016221/univ/art/502016221_univ_sqr_xl.jpg