Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Farao (1513 B.C.E.)

Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zambiri za Farao wa ku Iguputo amene anakanitsitsa kumvera Yehova. Sindikizani, dulani, pindani pakati ndipo sungani.