Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Potifara

Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti mudziwe za Potifara, yemwe anali Mwiguputo amene anagula Yosefe kuti akhale kapolo wake. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.