Phunziro 25: Mmene Mungapezere Anzanu
Anzanu enieni akhoza kukhala amsinkhu uliwonse ngati amakonda Yehova. Kodi anzanu ndi ndani?
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.