Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Phunziro 17: Tetezani Ana Anu

Phunziro 17: Tetezani Ana Anu

 

Makolo, tetezani ana anu ku zinthu zoipa.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.