Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kupilira Imfa ya Munthu Yemwe Munkamukonda

Kupilira Imfa ya Munthu Yemwe Munkamukonda

Timakhumudwa kwambiri munthu amene tinkamukonda akamwalira. Koma Yehova amatithandiza. Tiyeni tione mmene amatithandizira.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.