Kodi Zithunzizi Zikusiyana Pati?: Zochita Zokhudza Misonkhano
Pezani zinthu zomwe zikusiyana pa zithunzi ziwirizi. Kodi ndi chithunzi chiti chimene chikusonyeza khalidwe limene muyenera kusonyeza?
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.