Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA

Aisiraeli Analowa M’dziko la Kanani

Pangani dawunilodi makadiwa ndipo muyesere kufananitsa anthu otchulidwa m’Baibulo omwe ali m’buku la Yoswa chaputala 2 mpaka 7 ndi zinthu zokhudza anthuwo zimene zafotokozedwa.