Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kulera Ana

Zimene Mungachite Kuti Mukhale Mayi Kapena Bambo Wabwino

Kuti Banja Liziyenda Bwino​—Kupereka Chitsanzo

Kuti ana anu azitsatira zimene mumawaphunzitsa, zimene mumanena zizigwirizana ndi zimene mumachita.

Kuphunzitsa

Zimene Mungachite Pophunzitsa Mwana Wanu

Muyenera kuthandiza ana kumvetsa malamulo anu komanso zifukwa zimene mumawalangira.

Tetezani Ana Anu

Kalebe ndi sofiya akuphunzira zimene angachite kuti akhale otetezeka.