Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pemphero

Why Pray?

Kodi Mulungu Amamva Mapemphero Athu?

Baibulo limatitsimikizira kuti Mulungu amamvetsera mapemphero athu tikamapemphera m’njira yovomerezeka.

‘Muzimutulira Nkhawa Zanu Zonse’

Kodi muyeneradi kupemphera kwa Mulungu n’kumuuza nkhawa zanu? Kodi pemphero lingathandize bwanji anthu amene akuvutika ndi nkhawa?

Pemphero

Kodi Mungatani Kuti Mulungu Azimvetsera Mapemphero Anu?

Tikhoza kulankhula ndi Mulungu kulikonse, nthawi iliyonse, mokweza kapenanso chamumtima. Ndipotu Yesu anatithandiza kudziwa zomwe tinganene popemphera.

Kodi Mulungu Amamvetsera Mapemphero Onse?

Nanga bwanji ngati munthu akupempha zinthu zinazake chifukwa cha dyera? Bwanji ngati mwamuna atamenya mkazi wake, kenako n’kumapempha Mulungu kuti amudalitse?

Kodi Ndizipemphera kwa Anthu Oyera Mtima?

Dziwani zimene Baibulo limanena pa nkhani yakuti tizipemphera kwa ndani.