Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Chikhulupiro Komanso Kulambira

Chipembedzo

Kodi Zipembedzo Zonse N’zofanana Ndipo Zimathandizadi Anthu Kudziwa Mulungu?

Mfundo ziwiri zofotokozedwa m’Baibulo zingatithandize kudziwa yankho la funsoli.

Pemphero

Kodi Ndizipemphera kwa Anthu Oyera Mtima?

Dziwani zimene Baibulo limanena pa nkhani yakuti tizipemphera kwa ndani.

Kupulumuka

Kodi Yesu Amatipulumutsa Bwanji?

N’chifukwa chiyani Yesu amafunika kuchonderera m’malo mwathu? Kodi kungokhulupirira Yesu n’kokwanira kuti tidzapulumuke?

Kodi Nsembe ya Yesu Imawombola Bwanji “Anthu Ambiri”?

Kodi dipo limawombola bwanji anthu ku uchimo?

Kodi Ubatizo N’chiyani?

Kodi munthu amayenera kubatizidwa bwanji, nanga ayenera kubatizidwa liti? Kodi ubatizo umayeretsa machimo a munthu? Kodi ubatizo ndi ubatizo wa makanda umasiyana bwanji?

Kuchimwa Komanso Kukhululuka

Kodi Tchimo N’chiyani?

Kodi machimo ena amakhala aakulu kuposa ena?

Kodi Baibulo Limanena Kuti Kumwa Mowa Ndi Tchimo?

Baibulo limasonyeza kuti mowa ukhoza kuthandiza munthu amene akudwala m’mimba komanso likhoza kuthandiza munthu kuti azisangalala.

Zimene Zipembedzo Zimaphunzitsa

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kupatsa?

Kodi Mulungu amasangalala ndi kupatsa kotani?