Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Baibulo

MAFUNSO ENANSO A ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA...

Kodi Baibulo Linasinthidwa Kapena Kusokonezedwa?

Popeza kuti Baibulo ndi buku lakalekale, kodi tingatsimikize bwanji kuti uthenga wake ndi wolondola mpaka pano?

Kodi Sayansi Imagwirizana ndi Baibulo?

Kodi m’Baibulo muli mfundo zolakwika zokhudza sayansi?

Ulosi Komanso Zimene Ukuimira

Kutha kwa Dziko

Kodi Chizindikiro cha “Masiku Otsiriza” Kapena Kuti ‘Nthawi ya Mapeto’ N’chiyani?

Baibulo limafotokoza zinthu zosiyanasiyana zimene zidzachitika “mapeto a dziko” asanafike.

Kodi Nkhondo ya Aramagedo Idzakhala Yotani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibulo, koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imatchulidwa m’Baibulo lonse.

Kodi Dzikoli Lidzatha?

Baibulo limafotokoza bwino chifukwa chimene Mulungu analengera dziko lapansili

Anthu, Malo ndi Zinthu

Kodi Tingaphunzire Chiyani kwa Akazi Otchulidwa m’Baibulo?

Onani kusiyana kwa akazi omwe anachita zinthu mokhulupirika ndi akazi omwe anachita zoipa ndipo ndi zitsanzo zosafunika kutengera.

Kodi “Anzeru a Kum’mawa” Anali Ndani? Kodi Mulungu Ndi Amene Anawachititsa Kuti Alondole Nyenyezi ya ku Betelehemu?

Miyambo yambiri yomwe imachitika yokhudza Khirisimasi siipezeka n’komwe m’Baibulo.

Kodi Nkhani ya Nowa Komanso Chigumula Ndi Nthano Chabe?

Baibulo limafotokoza kuti Mulungu anabweretsa chigumula kuti awononge anthu oipa. Kodi Baibulo lili ndi umboni wotani wotsimikizira kuti linalembedwadi ndi Mulungu?

Kodi Mulungu Anasintha Zamoyo Zina Polenga Mitundu Inanso ya Zamoyo?

Baibulo silitsutsa zimene asayansi amanena zoti mitundu ya zamoyo imatulutsanso zamoyo zina zofanana ndi zamtundu womwewo.

Malangizo Othandiza

Kodi Ndalama ndi Zimene Zimabweretsa Mavuto Onse?

Zimene anthu ambiri amakonda kunena zoti “ndalama ndi muzu wa zoipa zonse,” zimangosonyeza kuti samvetsa zimene Baibulo limafotokoza.

Kodi Baibulo Lingandithandize Kupirira Matenda?

Inde. Onani mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kuti mupirire matenda.